Wxll Stephens – Low (Bonus) Lyrics

Wxll Stephens

Heyyy!
Codybeats

Ndimango yaka yaeee Ndimango yaka
Mm Ndimango banda… X2

Hook
Ndimango fatsa
Ndimango dekha
Ndili pa low
Ndimangoyaka, Ndimango banda
Ndili pa low!
Ndili pa low X5

It\’s my best day
Tipote ti bande
Minyama tichotse
Moto tiyatse eeh
Tipatse plan eeh
Tipatse Brandy
Tiyake to blande
Kaya ndi Monday
Likhala Friday
Rezin Gang Gang
Ati
Ngini tikupanga zikufwamba zikutheka X3
Ngini tikupanga
(Nkona ndikuti)

Hook
Ndimangoyaka, Ndimango banda
Ndili pa low!
Ndili pa low X5

Leave a Comment

Your email address will not be published. Required fields are marked *